Flag of Malawi Flag of Zambia Flag of Zimbabwe

CHICHEWA ( CHEWA, Cheva, Sheva )

A dialect of Nyanja spoken in Malawi. Also in Zambia and Zimbabwe.
Linguistic Lineage for Nyanja
Malawi - Zambia - Zimbabwe

Atate athu, muli mwamba,
Dzina lanu liyeretsedwe.
Ufumu wanu udze.
Kufuna kwanu kucitidwe,
Monga kumwamba choncho pansi pano.
Mutipatse lero chakudya chathu chalero.
Mutikhululukire zochimwa zathu.
Monga ifenso tikhululukira adani athu.
Musatisiye ife muchinyengo.
Koma mutipulumutse ife kwa zoyipa.
Amen.

Contributed by Anonymous - E-mail smuyebe@yahoo.com

Another version - 1981

Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, The Bible Societies Central Africa, 1981.

Atate wathu wa Kumwamba,
Dzina lanu liyeretsedwe.
Ufumu wanu udze.
Kufuna kwanu kuchitidwe, monga Kumwamba chomwecho pansi pano.
Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero.
Ndipo mutikhululukire ife mangawa athu,
monga ifenso takhululukira amangawa athu.
Ndipo musatitengere ife kokatiyesa,
koma mutipulumutse ife kwa woipayo
[chifukwa wanu uli ufumu ndi mphamvu ndi ulemerero, kwa nthawi zonse].
Amen.

Source: Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, The Bible Societies Central Africa, 1981.
Contributed by Aleksandr Ermanov, Rostov-na-Donu, Russia - E-mail ermanov@donpac.ru

Hail Mary!

Tinione Maria,
Wachaulere chodzaza,
Ambuye ali nanu.
Ndinu wodala mwa akazi onse
Wodalanso ndi mwana wanu Yesu.

Maria oyera,
Amayi a Mulungu,
Mutipempherere ife ochimwa
Tsopano ndi panthawi yakufa kwathu.
Amen.

Contributed by Anonymous - E-mail smuyebe@yahoo.com

SECTION INDEX CONVENT OF PATER NOSTER CHRISTUS REX

© Copyright Christus Rex, Inc.